Mboni za Yehova Padziko Lonse

Moldova

Mfundo Zachidule—Moldova

  • 2,978,000—Chiwerengero cha anthu
  • 17,979—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 195—Mipingo
  • Pa anthu 167 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA

Ndife Osauka Koma Olemera Mwauzimu

Zimene zinamuchitikira Alexander Ursu zinamuthandiza kudziwa kuti munthu akhoza kupita patsogolo mwauzimu ngakhale atakumana ndi mavuto ngati amene anthu omwe anali pansi pa ulamuliro wa Soviet Union anakumana nawo. Werengani nkhani yochititsa chidwiyi kuti mumve zimene anakumana nazo.