Mboni za Yehova Padziko Lonse

Latvia

  • Mzinda wa Riga, M’dziko la Latvia—Akusonyeza anthu mmene angagwiritsire ntchito webusaiti ya jw.org

Mfundo Zachidule—Latvia

  • 1,883,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,135—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 29—Mipingo
  • Pa anthu 898 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA

Lonjezo la Paradaiso Linasintha Moyo Wanga

Ivars Vigulis anali katswiri wa mpikisano woyendetsa njinga yamoto. Kodi ataphunzira Baibulo anayamba kuiona bwanji ntchito yakeyi?