Mboni za Yehova Padziko Lonse

Sri Lanka

  • Hatton, Sri Lanka​—Akugawira kabuku kofotokoza nkhani za m’Baibulo kwa munthu amene akuthyola tiyi

Mfundo Zachidule—Sri Lanka

  • 22,181,000—Chiwerengero cha anthu
  • 7,003—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 98—Mipingo
  • Pa anthu 3,195 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Zimene Ena Ali Nazo Zimathandizira pa Zimene Ena Akusowa

Kodi mayiko amene amapeza ndalama zochepa amathandizidwa bwanji kuti ntchito yathu iziyenda bwino?

NKHANI

Msonkhano Wapadera Woyamba Kuchitikira ku Sri Lanka

A Mboni za Yehova masauzande ambiri ochokera m’mayiko 7 anakumana ndi abale ndi alongo awo auzimu ku Colombo pamsonkhano wapadera, ndipo umenewu unali woyamba kuchitikira ku Sri Lanka.

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015

Mwambo Wotsegulira Ofesi ya Nthambi ku Sri Lanka

Anthu m’madera osiyanasiyana anatha kuonera pulogalamuyi m’masikirini.