Mboni za Yehova Padziko Lonse

Kazakhstan

Mfundo Zachidule—Kazakhstan

  • 19,899,000—Chiwerengero cha anthu
  • 17,287—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 229—Mipingo
  • Pa anthu 1,164 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

GALAMUKANI!

Dziko la Kazakhstan

Kale, anthu a ku Kazakhstan ankakonda kusamukasamuka komanso kukhala m’nyumba zotha kuyenda nazo. Kodi zimene anthuwa amachita masiku ano zikusonyeza bwanji kuti amakondabe chikhalidwe cha makolo awo?