Mfundo Zachidule—Kyrgyzstan
- 7,038,000—Chiwerengero cha anthu
- 5,167—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 86—Mipingo
- Pa anthu 1,387 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Zinthu Zonse N’zotheka ndi Yehova
Mawu ochepa amene mayi wina anamva m’basi anathandiza kuti moyo wa banja lake usinthiretu.
GALAMUKANI!
Dziko la Kyrgyzstan
Anthu a ku Kyrgyzstan ndi ochereza komanso aulemu. Kodi amatsatira miyambo yanji yokhudza banja?