Mfundo Zachidule—Japan
- 124,752,000—Chiwerengero cha anthu
- 214,457—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 2,888—Mipingo
- Pa anthu 583 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Uthenga Wabwino Unayamba Kuwala ku Japan
Makalavani otchedwa Yehu ankathandiza kwambiri polalikira uthenga wa Ufumu ku Japan.