Mboni za Yehova Padziko Lonse

Guyana

Mfundo Zachidule—Guyana

  • 798,000—Chiwerengero cha anthu
  • 3,280—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 46—Mipingo
  • Pa anthu 249 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

ZOCHITIKA PA MOYO

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Guyana

Kodi tingaphunzire zotani kwa anthu amene anatumikirapo kumene kukufunika olalikira ambiri? Kodi zimene iwo ananena zingakuthandizeni bwanji kukonzekera kukatumikira kudziko lina ngati mukufuna kutero?