Mfundo Zachidule—Guadeloupe
- 396,000—Chiwerengero cha anthu
- 8,488—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 118—Mipingo
- Pa anthu 47 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho
Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.