Mboni za Yehova Padziko Lonse

France

  • Paris, France​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo pafupi ndi mtsinje wa Seine

Mfundo Zachidule—France

  • 64,793,000—Chiwerengero cha anthu
  • 138,133—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,461—Mipingo
  • Pa anthu 474 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

“Yehova Anakubweretsani ku France Kuti Muphunzire Baibulo”

Mu 1919 dziko la France linalola kuti anthu a ku Poland asamukire m’dzikolo ndipo izi zinathandiza kuti ena aphunzire Baibulo.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

“Musalole Kuti Chilichonse Chikulepheretseni”

Atumiki a nthawi zonse a ku France a zaka za m’ma 1930 anali zitsanzo pa nkhani ya kudzipereka komanso kupirira.