Mboni za Yehova Padziko Lonse

Ethiopia

  • M’mudzi wa Tis Abay ku Ethiopia​—Akugawira kabuku kofotokoza nkhani za m’Baibulo ka chilankhulo cha Amharic

Mfundo Zachidule—Ethiopia

  • 123,771,000—Chiwerengero cha anthu
  • 11,512—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 206—Mipingo
  • Pa anthu 11,053 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Yehova Wandidalitsa Kuposa Mmene Ndinkaganizira

Kuchita umishonale ku Africa kunathandiza Manfred Tonak kuti akhale ndi makhalidwe abwino ambiri monga kuleza mtima komanso moyo wosalira zambiri.