Mboni za Yehova Padziko Lonse

Estonia

Mfundo Zachidule—Estonia

  • 1,366,000—Chiwerengero cha anthu
  • 4,110—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 54—Mipingo
  • Pa anthu 335 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NTCHITO YOFALITSA MABUKU

Dziko la Estonia Linayamikira Kwambiri Baibulo la Dziko Latsopano

M’chaka cha 2014, dziko la Estonia linaika Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika m’gulu la zinthu zomwe zinalembedwa bwino kwambiri m’chaka chimenecho.