Mboni za Yehova Padziko Lonse

Dominican Republic

  • Mumzinda wa Samaná ku Dominican Republic—Akuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo kwa munthu wogulitsa kokonati

Mfundo Zachidule—Dominican Republic

  • 11,156,000—Chiwerengero cha anthu
  • 38,792—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 536—Mipingo
  • Pa anthu 293 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015

Dominican Republic

Werengani nkhani yosangalatsa yokhudza Mboni za Yehova ku Dominican Republic.