Mboni za Yehova Padziko Lonse

Denmark

  • Ebeltoft, Denmark—Akugawira kapepala kakuti Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala?

Mfundo Zachidule—Denmark

  • 5,941,000—Chiwerengero cha anthu
  • 14,639—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 172—Mipingo
  • Pa anthu 410 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni za Yehova Athandiza Achipatala Kupanga Opaleshoni Odwala Popanda Kuwapatsa Magazi ku Denmark

Ofalitsa nkhani ambiri odziwika bwino ananena kuti ku Denmark, zipatala zambiri zinayamba kupanga anthu opaleshoni popanda kugwiritsa ntchito magazi.