Mboni za Yehova Padziko Lonse

Cuba

  • Havana, Cuba​—Kulalikira nyumba ndi nyumba mumzinda wa Old Havana

Mfundo Zachidule—Cuba

  • 11,090,000—Chiwerengero cha anthu
  • 87,907—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,366—Mipingo
  • Pa anthu 129 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi