Mboni za Yehova Padziko Lonse

Cameroon

  • Buea, Cameroon​—Kulalikira munthu amene akuthyola tiyi pafupi ndi phiri la Cameroon

Mfundo Zachidule—Cameroon

  • 28,608,000—Chiwerengero cha anthu
  • 44,558—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 500—Mipingo
  • Pa anthu 665 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Ntchito Yomanga Inayenda Bwino Mliri Usanayambe

Tinakonza zoti timange kapena kukonzanso malo olambirira oposa 2,700 m’chaka cha utumiki cha 2020. Kodi mliri wa COVID-19 unakhudza bwanji zimenezi?

GALAMUKANI!

Dziko la Cameroon

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mbiri komanso chikhalidwe cha anthu a ku Cameroon.