Mfundo Zachidule—Switzerland
- 8,813,000—Chiwerengero cha anthu
- 20,024—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 258—Mipingo
- Pa anthu 445 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
KALE LATHU
Anapereka Zinthu Zawo Zabwino Kwambiri
Kodi a Mboni za Yehova anathandiza bwanji abale awo a ku Germany nkhondo yachiwiri yapadziko lonse itangotha?
KALE LATHU
Anapereka Zinthu Zawo Zabwino Kwambiri
Kodi a Mboni za Yehova anathandiza bwanji abale awo a ku Germany nkhondo yachiwiri yapadziko lonse itatangotha?