Mboni za Yehova Padziko Lonse

Congo (Brazzaville)

Mfundo Zachidule—Congo (Brazzaville)

  • 5,941,000—Chiwerengero cha anthu
  • 9,517—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 123—Mipingo
  • Pa anthu 661 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KUTHANDIZA ENA

Pa Nthawi ya Tsoka, Timathandizana Chifukwa cha Chikondi

M’mayiko ambirimbiri, a Mboni za Yehova amathandiza anthu amene ali m’mavuto.