Mboni za Yehova Padziko Lonse

Congo (Kinshasa)

Mfundo Zachidule—Congo (Kinshasa)

  • 98,152,000—Chiwerengero cha anthu
  • 257,672—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 4,385—Mipingo
  • Pa anthu 402 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni za Yehova Anapereka Chithandizo kwa Anthu Othawa Nkhondo ku Congo

A Mboni za Yehova akupereka chithandizo kwa Akhristu anzawo komanso anthu ena omwe anathawa nkhondo m’chigawo cha Kasai ku Democratic Republic of the Congo.

NTCHITO YOFALITSA MABUKU

Ntchito Yotumiza Mabuku ku Congo

A Mboni za Yehova amayenda mtunda wautali mwezi uliwonse kuti akasiye Mabaibulo ndiponso mabuku kwa anthu a m’dziko la Congo.