Mboni za Yehova Padziko Lonse

Australia

  • Wollongong ku New South Wales, Australia—Akugawira kapepala koitanira anthu ku misonkhano

Mfundo Zachidule—Australia

  • 26,636,000—Chiwerengero cha anthu
  • 71,188—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 726—Mipingo
  • Pa anthu 379 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KUTHANDIZA ENA

A Mboni Akulimbikitsa ndi Kutonthoza Okalamba

A Mboni za Yehova amayendera okalamba omwe ali kunyumba zosungira okalamba ku Australia.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka Ndi Mtima Wonse ku Oceania

Kodi a Mboni za Yehova amene anasamukira komwe kulibe ofalitsa ambiri ku Oceania amatani akakumana mavuto?

KUTHANDIZA ENA

A Mboni za Yehova Analandira Ulemu Chifukwa Chothandiza Akaidi

A Mboni za Yehova anagwira ntchito yofunika kwambiri yothandiza akaidi m’dziko la Australia kumalo ena aakulu kwambiri osungirako anthu olowa m’dzikolo mopanda chilolezo. Kodi ntchito yake mukuidziwa?

NTCHITO YOLALIKIRA

Kulalikira M’dera Lakutali​—Australia

Onerani vidiyo yosonyeza banja lina la Mboni za Yehova likulalikira uthenga wa m’Baibulo kwa anthu a kudera lakutali m’dziko la Australia.