Mfundo Zachidule—Argentina
- 46,045,000—Chiwerengero cha anthu
- 153,751—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 1,938—Mipingo
- Pa anthu 301 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
Malo Atsopano Osungirako Zinthu Zakale Atsegulidwa Ku Ofesi ya Nthambi ya Argentina
Malowa ali ndi mbali ziwiri zokhala ndi mitu yakuti, “Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo” komanso “Mawu Anu Adzakhalapo Mpaka Kalekale.”
NKHANI
Ntchito Yayikulu Yolalikira Inachitika pa Nthawi ya Mpikisano wa Olympic wa Masewera a Achinyamata ku Argentina
Abale athu ankagawira mabuku pafupifupi 800 pa tsiku pa nthawi yomwe ankalalikira kwa achinyamata omwe ankachita masewera komanso kwa alendo.