Mboni za Yehova Padziko Lonse

Andorra

  • Mzinda wa Andorra la Vella m’dziko la Andorra​—Akuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? m’chilankhulo cha Chikatalani

Mfundo Zachidule—Andorra

  • 84,000—Chiwerengero cha anthu
  • 174—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 3—Mipingo
  • Pa anthu 509 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi