Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa YAMBANI Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa Kodi timadziwa bwanji kuti Mulungu amakhudzidwa tikaferedwa munthu amene tinkamukonda? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi GALAMUKANI! Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa Baibulo lili ndi mfundo zolimbikitsa, zopereka chiyembekezo komanso zothandiza anthu amene okondedwa awo anamwalira. KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi M’Baibulo Mungapezemo Mawu Omwe Angakulimbikitseni? Mawu a m’Baibulo alimbikitsa anthu ambiri omwe akulimbana ndi mavuto ena ake komanso omwe amavutika maganizo chifukwa cha mavuto. NKHANI ZINA Zimene Mungachite Mukaferedwa Muone zinthu zimene zingakuthandizeni kupirira. NSANJA YA OLONDA Kodi Pangakhalenso Chifukwa Chokhalira Ndi Moyo Munthu Amene Timamukonda Akamwalira? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 5 zimene mungachite kuti muthe kupirira imfa ya munthu amene munkamukonda. KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Mawu Akuti Kuuka kwa Akufa Amatanthauza Chiyani? Mungadabwe mutadziwa zimene Baibulo limanena zokhudza anthu amene adzaukitsidwe. ZOKHUDZA IFEYO Pemphani Kuti Tidzakuyendereni Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa NKHANI ZINA Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa Chichewa Uthenga Wotonthoza Anthu Omwe Aferedwa https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/501100047/univ/art/501100047_univ_sqr_xl.jpg mrt article 54