Baibulo Lomwe Linasowa Lapezekanso
Akatswiri ochita kafukufuku apeza mipukutu yofunika kwambiri ya Baibulo yomwe anthu ankaganiza kuti inawonongeka.