Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mmene Zamoyo Zinapangidwira

Mmene Zamoyo Zinapangidwira

Kodi pali winawake amene anapangitsa kuti kukhale zinthu zamoyo? Chamoyo chilichonse chimadalira chamoyo chinzake m’njira inayake.