NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) March 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira May 6–​June 9, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 9

Kodi Ndinu Okonzeka Kudzipereka kwa Yehova?

Idzaphunziridwa mlungu wa May 6-12, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 10

‘Pitirizani Kutsatira’ Yesu Mukabatizidwa

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 13-19, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 11

Mukhoza Kumatumikirabe Yehova Ngakhale Mutakhumudwitsidwa

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 20-26, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 12

Musakhale Mumdima, Koma Khalanibe M’kuwala

Idzaphunziridwa mlungu woyambira May 27–​June 2, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 13

Musamakayikire Kuti Yehova Amasangalala Nanu

Idzaphunziridwa mlungu woyambira June 3-9, 2024.

Kukhululuka Machimo Amene Anachitika Kale

Kodi Yehova akanakhululuka bwanji machimo amene anachitika dipo lisanaperekedwe n’kukhalabe Mulungu wachilungamo?