NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) January 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira March 4–April 7, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 1

Mukamachita Mantha, Muzidalira Yehova

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 4-10, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 2

Kodi Mwakonzeka Kudzapezekapo pa Tsiku Lofunika Kwambiri pa Chaka?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 11-17, 2024.

Kodi Mumaona Akazi Ngati Mmene Yehova Amawaonera?

Ngakhale m’bale atakulira m’chikhalidwe chotani, angathe kuphunzira komanso kutsanzira mmene Yehova amachitira pokonda komanso kulemekeza akazi.

Kodi Mukudziwa?

Kodi nduna ya ku Itiyopiya inakwera galeta lotani pomwe inakumana ndi Filipo?

NKHANI YOPHUNZIRA 3

Yehova Adzakuthandizani pa Nthawi Yovuta

Idzaphunziridwa mlungu woyambira March 25-31, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 4

Yehova Amakukondani Kwambiri

Idzaphunziridwa mlungu wa April 1-7, 2024.