NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) February 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira April 8–May 5, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 5

‘Sindidzakutayani Ngakhale Pang’ono’

Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 8-14, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 6

“Tamandani Dzina la Yehova”

Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 15-21, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 7

Zimene Tingaphunzire kwa Anaziri

Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 22-28, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 8

Pitirizani Kutsatira Malangizo a Yehova

Idzaphunziridwa mlungu woyambira April 29–​May 5, 2024.

Muzisangalala Pamene Mukuyembekezera Yehova Moleza Mtima

Anthu ambiri amafooka ndi mavuto a m’dzikoli pamene akuyembekezera nthawi yoti Yehova athetse mavutowo. N’chiyani chingathandize kuti kuyembekezerako kukhale kosavuta komanso kuti tizisangalala pamene tikuyembekezera?

Abale Awiri Atsopano M’Bungwe Lolamulira

Lachitatu pa 18 January 2023, panalengezedwa kuti M’bale Gage Fleegle ndi M’bale Jeffrey Winder aikidwa kuti azitumikira m’Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi Baibulo limafotokoza zotani zokhudza Yehova pa nkhani yoneneratu zam’tsogolo?

Kodi Mukudziwa?

Taonani mfundo zitatu zimene ziyenera kuti zinachititsa olemba Baibulo kuchita zimenezi.