NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2023

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira February 5–March 3, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 50

Chikhulupiriro Komanso Ntchito Zake Zingachititse Kuti Tikhale Olungama

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa February 5-11, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 51

Tili ndi Chiyembekezo Chomwe Sichitikhumudwitsa

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa February 12-18, 2024.

Kodi Mumayendera Maganizo a Yehova pa Nkhani ya Mowa?

Ena amasankha kumwa mowa pomwe ena amakana. Kodi n’chiyani chingakuthandizeni kuti mupewe mavuto amene amabwera chifukwa cha kumwa mowa?

NKHANI YOPHUNZIRA 52

Akhristu Achitsikana, Kodi Mungatani Kuti Mukhale Olimba Mwauzimu?

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa February 19-25, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 53

Akhristu Achinyamata, Kodi Mungatani Kuti Mukhale Olimba Mwauzimu?

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa February 26–​March 3, 2024.

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga mosamala magazini a chaka chino a Nsanja ya Olonda? Taonani zimene mukukumbukira.

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2023

Mlozera nkhani wa nkhani zonse zotuluka m’magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2023, ndipo zalembedwa motsatira mitu yake.

Zochitika

Kodi mlongo wina anasonyeza bwanji chifundo pofufuza mipata yoti alalikire anthu ena?