GALAMUKANI! Na. 2 2020 | Mayankho a Mafunso 5 Okhudza Kuvutika

Kuphunzira Baibulo kungakutonthozeni pamene mwakumana ndi mavuto.

Zimene Ena Amakhulupirira

Onani zimene zipembedzo zosiyanasiyana zimanena pa nkhani ya chifukwa chake timavutika.

1 Kodi Mulungu ndi Amene Amachititsa Kuti Tizivutika?

Anthu ambiri amasokonezedwa ndi ziphunzitso zabodza zokhudza Mulungu. Kodi zoona zake ndi ziti?

2 Kodi Mavuto Athu Timawachititsa Tokha?

Ngati yankho ndi lakuti inde, ndiye kuti tikhoza kukwanitsa kuchepetsako mavuto athu.

3 N’chifukwa Chiyani Anthu Abwino Amavutika?

Baibulo limatithandiza kudziwa chifukwa chake.

4 Kodi Tinalengedwa Kuti Tizivutika?

Kodi Mulungu amene analenga zinthu zokongola zonsezi, angalenge anthufe kuti tizivutika? Ngati sangatero, ndiye kodi chinalakwika n’chiyani?

5 Kodi Kuvutika Kudzatha?

Baibulo limatifotokozera mmene Mulungu adzathetsere mavuto.

Mungapeze Thandizo

Ngakhale zitaoneka ngati mavuto athu sangathe, pali malangizo odalirika omwe angatithandize.