Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale​—Yambani Kuphunzira Baibulo

Kabukuka kakuthandizani kuti muyambe kuphunzira Baibulo ngati njira imene timagwiritsa ntchito pophunzira Baibulo ndi anthu kwaulere.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi Phunziro la Baibulo lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?

Mukamaphunzira Baibulo kwaulere ndi a Mboni za Yehova, mungagwiritse ntchito Baibulo lililonse limene mukufuna. Mungapemphenso onse a m’banja lanu kapena mnzanu wina aliyense kuti akhale nanu pa phunzirolo.