N’ciani Catsopano?

2024-05-31

KHALANI MASO!

Kuwonjezeka kwa Kusamvela Malamulo Padziko Lonse—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Dziwani cimene cikupangitsa kusamvela malamulo kumene tikuona padziko lonse.

2024-05-20

KHALANI MASO!

Makhalidwe Aloŵa Pansi—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Makhalidwe aloŵa pansi kwambili kuposa n’kale lonse. Baibo imafotokoza cifukwa cake ndipo imapeleka malangizo odalilika amene angathandize kuti tizikhala aulemu m’zokamba na zocita zathu.

2024-05-09

NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA

“Uthenga Wabwino”! (Nyimbo ya pa Msonkhano Wacigawo wa 2024)

Kuyambila m’zaka za zana loyamba mpaka masiku ano, mwacimwemwe anthu akhala akulalikila uthenga wabwino. Uthengawo ni wofunika kwambili kuposa uthenga wina ulionse cifukwa umakamba za nchito imene Yesu iye mwini anaiyambitsa, komanso mmene angelo amamuthandizila pa nchitoyi.