Onani zimene zilipo

Baibo ya pa Intaneti

Ŵelengani na kumvetsela ku Baibo pa intaneti, kapena citani daunilodi kwaulele zomvetsela kapena mavidiyo aulele a m’citundu ca manja. Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika ni yolondola, ndiponso yosavuta kuŵelenga. Inafalitsidwa yonse yathunthu, kapena mbali yake cabe, mu vitundu vopitilila 160. Ndipo makope oposa 220 miliyoni apulutidwa.

ONANI

BAIBO YA CIMASULILO CA DZIKO LATSOPANO