Pitani ku nkhani yake

Achinyamata

Mayina a anthu ena amene atchulidwa m’nkhanizi asinthidwa.

ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA

N’chifukwa Chiyani Ndikufunika Kumathandiza Ena?

Kuchitira ena zabwino kumakuthandizani m’njira ziwiri. Kodi njira zimenezi ndi zotani?

ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA

N’chifukwa Chiyani Ndikufunika Kumathandiza Ena?

Kuchitira ena zabwino kumakuthandizani m’njira ziwiri. Kodi njira zimenezi ndi zotani?

Zimene Achinyamata Amafunsa

Mafunso amene achinyamata amafunsa pa nkhani zokhudza kugonana, anthu ocheza nawo, makolo, sukulu ndi zina zambiri.

Zimene Achinyamata Anzanu Amanena

Mwina mukukumana ndi mavuto omwe simunakumanepo nawo chiyambire. Onani zimene anzanu amachita pothana ndi mavutowo.

Mavidiyo Amakatuni

Kodi munakumanapo ndi vuto linalake limene munaona kuti ndi losatheka kuthana nalo? Mavidiyo amenewa angakuthandizeni kuthana ndi mavuto ambiri omwe achinyamata ambiri amakumana nawo.

Zoti Achinyamata Achite

Mapepalawa angakuthandizeni kuti mukonzekere ndi kulemba zimene mungachite ngati mutakumana ndi vuto limene latchulidwa papepalalo.

Kodi Mukuphunzira Chiyani pa Nkhani ya M’Baibulo Iyi

Nkhani za m’Baibulozi, zomwe mungathe kuzisindikiza zingakuthandizeni ngati mutaziphunzira mozama.

Mayankho a Mafunso 10 Omwe Achinyamata Amadzifunsa

Pezani malangizo othandiza kuti zinthu zikuyendereni bwino.

Zokuthandizani Pophunzira

Gwiritsani ntchito zokuthandizani pophunzira kuti musamakaikire zimene mumakhulupirira komanso kuti mudziwe mmene mungazifotokozere kwa ena.