Onani zimene zilipo

Zimene Baibo Imaphunzitsa

Baibo imapeleka mayankho pa mafunso ofunika kwambili mu umoyo. Malangizo ake akhala odalilika kwa zaka mahandiledi. M’cigawo cino, mudzapeza cifukwa cake mungaidalile Baibo, mmene mungapindulile mukamaiŵelenga, komanso mudzaona mmene malangizo ake alili othandiza.—2 Timoteyo 3:16, 17.

 

Zimene Zilipo

KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBO

Kodi Chimo N’ciyani?

Kodi machimo ena amakhala aakulu kuposa ena?

KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBO

Kodi Chimo N’ciyani?

Kodi machimo ena amakhala aakulu kuposa ena?

Phunzilani Baibo

Pemphani kuti wa Mboni adzakucezeleni

Kambilanani nkhani ya m’Baibo na Mboni za Yehova, kapena laŵani maphunzilo a Baibo amene timapeleka.

Kodi Baibo Ingakuthandizeni Bwanji?

Zocita za Ana

Seŵenzetsani zocita zosangalatsazi, zozikika pa Baibo, pophunzitsa ana makhalidwe auzimu.

Kodi Baibo Imati Ciani?

Kuyankha Mafunso a m’Baibo

Pezani mayankho ocokela m’Baibo okhudza Mulungu, Yesu, banja, mavuto komanso ena ambili.