Pitani ku nkhani yake

Andrey Nesmachniy: Kusewera Mpira Kunali Chinthu Chofunika Kwambiri pa Moyo Wanga

Andrey Nesmachniy: Kusewera Mpira Kunali Chinthu Chofunika Kwambiri pa Moyo Wanga

Andrey atakwaniritsa maloto ake, zinthu zinasintha pa moyo wake ndipo zinamupangitsa kuyamba kukayikira za cholinga cha moyo. Koma mudabwa kuona komwe anapeza yankho la funso lake lokhudza cholinga cha moyo.