Zochitika pa Moyo wa a Mboni za Yehova

A Mboni za Yehova amayesetsa kulola kuti Baibulo lomwe ndi Mawu a Mulungu lizitsogolera maganizo, zoyankhula ndi zochita zawo. Onani mmene lawathandizira pa moyo wawo komanso pa moyo wa anthu ena.