Mbiri Komanso Baibulo

Baibulo ndi buku lapadera kwambiri tikaganizira zimene zinachitika kuti lisungidwe kwanthawi yaitali, limasuliridwe komanso kufalitsidwa. Zimene akatswiri apeza posachedwapa zikupitirizabe kutsimikizira kuti ndi lolondola. Mosaganizira za chipembedzo chanu, nanunso mungavomereze kuti Baibulo silingafanane ndi buku lina lililonse.

Laibulale

Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?

Kodi mfundo yaikulu yomwe imapezeka m’Baibulo ndi iti?