Baibulo Komanso Sayansi

Kodi Baibulo limagwirizana ndi zimene asayansi amaphunzitsa? Kodi Baibulo limanena zolondola pankhani za sayansi? Werengani zimene asayansi amanena komanso zimene chilengedwe chimasonyeza pankhani imeneyi.