Pitani ku nkhani yake

Zokhudza Mboni za Yehova Padziko Lonse

  • Mayiko amene a Mboni za Yehova amalambira Mulungu​—239

  • Mboni za Yehova padziko lonse​—8,816,562

  • Maphunziro a Baibulo aulere​—7,281,212

  • Anthu amene anapezeka pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu​—20,461,767

  • Mipingo​—118,177

 

Mboni za Yehova Padziko Lonse

Timapezeka padziko lonse ndipo timachokera m’mitundu komanso zikhalidwe zosiyanasiyana. Mwina mukudziwa kuti timagwira ntchito yolalikira koma timagwiranso ntchito zina zothandiza anthu a m’madera athu.