Pitani ku nkhani yake

Malo a Nkhani

 

NKHANI

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2024

Mu lipotili, tiona mmene Atate wathu wachikondi Yehova, amasonyezera kuti “akufuna kuti anthu onse alape.” (2 Pet. 3:9) Tionanso zinthu zina zimene zasintha pa nkhani ya mmene tiyenera kuvalira tikamachita zinthu zauzimu.

NKHANI

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2024

Mu lipotili, tiona mmene Atate wathu wachikondi Yehova, amasonyezera kuti “akufuna kuti anthu onse alape.” (2 Pet. 3:9) Tionanso zinthu zina zimene zasintha pa nkhani ya mmene tiyenera kuvalira tikamachita zinthu zauzimu.

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 1 la 2024

Onani mmene kukonda anthu kungatithandizire kuti tizichita khama mu utumiki.

Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2023

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza zimene abale athu akuchita posonyeza kuti akupanga Yehova kukhala malo awo othawirapo ngakhale kuti akukumana ndi mavuto.

2023-04-28

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2023

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti lokhudza abale ndi alongo athu a ku Türkiye komanso akucheza ndi abale awiri.

2023-01-09

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2023

Tikukulimbikitsani kuti muonere lipotili kuti mumve zilengezo zosangalatsa kwambiri zokhudza ntchito yomanga ya ku Ramapo komanso zokhudza apainiya.

2022-12-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tizikhala okonzeka kusintha kuti tiziyenda limodzi ndi galeta la Yehova.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tizikonzekereratu n’cholinga choti tidzachite zinthu mwamsanga tikadzakumana ndi tsoka.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 6 la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti la zinthu zina zomwe zachitika posachedwapa. Akulengezanso za lemba lachaka cha 2023.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 5 la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza zomwe zinathandiza abale ndi alongo kuti apirire pamene ankazunzidwa pa nthawi ya ulamuliro wa Soviet Union. Akufotokozanso mfundo zotitsimikizira kuti Yehova apitiriza kutithandiza.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tizikhalabe okhulupirika tikakumana ndi mayesero potsanzira abale athu akum’mawa kwa Europe.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zomwe zingatithandize kulimbana ndi nkhawa zomwe tingakhale nazo chifukwa cha nkhondo yomwe ikuchitika m’mayiko akum’mawa kwa Europe.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira, akufotokoza mmene abale ndi alongo akusonyezera kuti ndi okhulupirika ngakhale kuti akukumana ndi mayesero.

2022-11-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tipitirizebe kukhala maso mwauzimu.

2022-02-02

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 10 la 2021

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti lokhudza mliri wa COVID-19 komanso njira za mmene tingagwiritsire ntchito nthawi yathu mwanzeru

2022-01-04

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 9 la 2021

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zolimbikitsa komanso muli vidiyo yosonyeza zimene abale ndi alongo afotokoza zokhudza pulogalamu yongoyeserera yoyambiranso kusonkhana pamasom’pamaso.