Nyimbo Zachikhristu

Koperani nyimbo zachikhristu zabwino kwambiri, zomwe mungazigwiritse ntchito potamanda ndiponso polambira Yehova Mulungu. Zina mwa nyimbo zimenezi zili ndi mawu ndipo zina ndi zopanda mawu.

Sankhani chinenero chimene mukufuna pa kabokosi ka zinenero, kenako dinani kabatani ka Fufuzani kuti muone nyimbo zimene zilipo m’chinenerocho.

NYIMBO ZATHU

“M’dziko Labwino”

Kuganizira kwambiri za chiyembekezo chathu kumatithandiza kupirira ngakhale mavuto aakulu.

NYIMBO ZATHU

“M’dziko Labwino”

Kuganizira kwambiri za chiyembekezo chathu kumatithandiza kupirira ngakhale mavuto aakulu.