Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi Baibulo limaphunzitsa chiyani kwenikweni? Sankhani funso limene lakuchititsani chidwi pa mafunso ali m’munsiwa.

Kuphunzira Baibulo ndi Mboni za Yehova

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo—Vidiyo Yathunthu

Baibulo likuthandiza anthu ambirimbiri padziko lonse lapansi kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri. Kodi inunso mungakonde?

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.

Pemphani Kuti Tidzakuyendereni

Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova.